MARSTE X KELL KAY_MWANO
Martse ft kell kay _ Mwano ( prod. by tricky beats & ak )
Verse 1 ( Martse )
Maso anga pano anayamba mwano /
akazi enawa sakumasiliraso /
Popeza iwowo anapanga chisankho /
kuti ana_spota mmodzi ndipo alipo yekhayo /
Mutu wanga nawoso wayamba mwanotu /
akazi enawa sukuganizirako /
popeza iwowo unapanga chisankho /
kuti unafila mmodzi ndipo alipo yekhayo /
Kamtima kangakaso ndekayamba mwaanotu /
zokamba anthu ena sizimakawawasotu /
usanabwere iwe kadali kosweka /
pano kazitolera nde kayamba kudziva kubeba /
kapena mwina udandidyetsa mankhwala /
kumangokuganizira ndikangokhala /
kupanda kukuona ine mtima kuwawa /
tangobwera lero lomwe sindingandikile mpaka mawa /
Hook ( Kell kay )
ndizonse zanga /
mumtima mwanga ine /
sindipereka mpataso eeh mwano /
Kuti ndizonse zanga /
mumtima mwaanga /
sindipereka mpataso eeh mwano /
eeh mwano.eeeeh mwanoooo /
Verse 2 ( Martse )
ndati dekhani /
zipezeleni wanu wangayi ndati lekani /
ndisiyileni wangayu chonde ndati pepani /
Kumuveka mphete imeneyo nde yanga plan /
so you know wagwan!! /
Kamandikonda ngakhale ndilibe paper /
nkadzayiphula uziwe sindizakuleka /
wakonda mphawi ndipo anzako akuseka koma dziwa amadziwa zonse ndi Mulungu yekha /
Auzeni masteni ndawapezela in_law /
Auze mahope ako kuti suli single /
ndakhazikika and am not ready to mingle /
Zakupanga introduce kwa ma friend mpaka ku mpingo /
kapena mwina udAndidyetsa mankhwala /
kumangokuganizira ndikangokhala /
Kupanda kukuona ine mtima kuwawa /
tangobwela lero lomwe sindingadikile mpaka mawa /
Hook ( Kell kay )
ndizonse zanga /
mumtima mwanga ine /
sindipereka mpataso eeh mwano /
Kuti ndizonse zanga /
mumtima mwaanga /
sindipereka mpataso eeh mwano /
eeh mwano.eeeeh mwanoooo /
Bridge ( Kell kay )
Ndalimba mtima /
Kukonda iwe wekha /
Uli ndine uchotse mantha iwe dekha /
I got a plan for you and me /
Kamphete kokha ndidzakuveka /
Uli ndiine uchotse mantha iwe dekhaaaa /
Hook ( Kell kay )
ndizonse zanga /
mumtima mwanga ine /
sindipereka mpataso eeh mwano /
Kuti ndizonse zanga /
mumtima mwaanga /
sindipereka mpataso eeh mwano /
eeh mwano.eeeeh mwanoooo /
Post a Comment