Intro Hook
Ndiye yekha amene amandikwanira/
Palibe ofananaye/
Bwenzi langa sandikhumudwitsa/
Adziwa zinsinsi zapansi pa mtima wanga/
And his love will never end/
Ndiye yekha amene amandikwanira/
Palibe wofana naye/
Verse 1 ( Khetwayo)
Eh! Sitidzasiyana/
chikondi chathu ndi mpakana muyaya /
Ndichoposa lonjezano la banja /
Chimapyola sichothera kumanda/
Ndafunsafunsa ine ponse kuzungulira ngati Nguli Paliponse /
Chikondi chotere sinachione wachikondi wotere sin’damuone/
Ah!chikondi chopanda season mumtendere komanso muchisoni/
Chanthawi zonse chopanda nyengo katangale palibenso zachinyengo/
Andikonda alibe break/
Sadzandithawa palibe za heart break/
Hook (Lawi)
Ndili ndi bwenzi langa londikonda /
Bwenzi langa sandikhumudwitsa/
Adziwa zinsinsi zapansi pa mtima wanga/
And his love will never end/
Ndiye yekha amene amandikwanira/
Palibe ofana naye.
Verse 2 (Kbg)
Mtima wanga wakhala ukumango thyoledwa /
Amaitcha heart break opanda wondimenda /
"Mend my heart" (LAWI).. ndimafuula yesu nandimvera/
Ona pamtanda wandikonda mpaka wandifera/
Ha ndapata wachikondi wandipatsa chimwemwe kutsaya ngati ma dimples/
Chikondi chake paine eh chilibe pause/
Sichilingati series chopanda ma season/
Eya chikondi ndi unconditionally /
Satana nsanje kukhomerera ndi misomali /
Cholinga andisiye koma ichi ndi agape chopangitsa yo kuti abone ukamufunse nafe/
Makalata ndiye osanena walembalembanso/
Kuyambira genesis mpakana chivumbulutso/
Chiponse apa chikondi chopanada ma season ndibwenzi lofewa paiye ndagonekera khosi/
Hook (Lawi)
Ndili ndi bwenzi langa londikonda /
Bwenzi langa sandikhumudwitsa/
Adziwa zinsinsi zapansi pa mtima wanga/
And his love will never end/
Ndiye yekha amene amandikwanira/
Palibe ofana naye.
T-Shirt - T-Shirt - T-Shirt - T-Shirt Shop
ReplyDeleteT-Shirt - T-Shirt. by T-Shirt. T-Shirt. $15.99. Quantity. Add to titanium wok cart. Description. T-Shirt. T-Shirt. $15.99. Quantity. titanium pry bar Add columbia titanium to cart. Description. T-Shirt. T-Shirt. titanium fat bike $15.99. titanium shift knob Quantity. Add to cart. Description. T-Shirt.
read wholesale sex toys,dildos,vibrators,wholesale sex toys,realistic dildo,sex toys,sex chair,japanese sex dolls,wholesale sex toys Recommended Reading
ReplyDeletePost a Comment